Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo pomwepo analowa m'mangum'mangu kwa mfumu, napempha kuti, Ndifuna kuti mundipatse tsopano apa, mutu wake wa Yohane Mbatizi mumbale.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo pomwepo analowa m'mangum'mangu kwa mfumu, napempha kuti, Ndifuna kuti mundipatse tsopano apa, mutu wake wa Yohane Mbatizi mumbale.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Mtsikana uja adabwerera msanga kwa mfumu nanena kuti, “Ndifuna kuti tsopano pompano mundipatse mutu wa Yohane Mbatizi m'mbale.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Nthawi yomweyo mtsikana uja anafulumira kupita komwe kunali mfumu ndi pempho lake: “Ndikufuna kuti mundipatse pomwe pano mutu wa Yohane Mʼbatizi mʼmbale.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:25
8 Mawu Ofanana  

pakuti mapazi ao athamangira zoipa, afulumira kukhetsa mwazi.


chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake ndiko masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwirizo zodzala ndi ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta ukhale nsembe yaufa;


Ndipo iye, atampangira amake, anati, Ndipatseni ine kuno m'mbale mutu wa Yohane Mbatizi.


Ndipo masiku aja anadza Yohane Mbatizi, nalalikira m'chipululu cha Yudeya,


Ndipo anatuluka, nati kwa amake, Ndidzapempha chiyani? Ndipo iye anati, Mutu wake wa Yohane Mbatizi.


Ndipo mfumu inamva chisoni chachikulu; koma chifukwa cha malumbiro ake, ndi cha iwo akukhala pachakudya, sanafune kumkaniza.


miyendo yao ichita liwiro kukhetsa mwazi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa