Marko 6:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo anamlumbirira iye, kuti, Chilichonse ukandipempha ndidzakupatsa, kungakhale kukugawira ufumu wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo anamlumbirira iye, kuti, Chilichonse ukandipempha ndidzakupatsa, kungakhale kukugawira ufumu wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ndipo adatsimikiza molumbira kuti, “Chilichonse chomwe uti undipemphe, ndikupatsa ndithu, ngakhale kukudulira dziko langa lino pakati.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ndipo analonjeza ndi lumbiriro kuti, “Chilichonse chimene upempha ndidzakupatsa, ngakhale theka la ufumu wanga.” Onani mutuwo |