Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:19 - Buku Lopatulika

19 Ndipo Herodiasi anamuda, nafuna kumupha; koma sanakhoze;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ndipo Herodiasi anamuda, nafuna kumupha; koma sanakhoze;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Tsono Herodiasiyo ankadana naye Yohane, ndipo ankafuna kuti aphedwe basi. Koma ankalephera,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Ndipo Herodia anamusungira Yohane chidani ndipo anafuna kumupha, koma sanathe kutero,

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:19
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Ahabu anati kwa Eliya, Wandipeza kodi, mdani wangawe? Nayankha, Ndakupeza; pokhala wadzigulitsa kuchita choipacho pamaso pa Yehova.


Usakangaze mumtima mwako kukwiya; pakuti mkwiyo ugona m'chifuwa cha zitsiru.


Iwe waona zinthu zambiri, koma susamalira konse; makutu ako ali otseguka, koma sumva konse.


Pakuti Herode adamgwira Yohane, nammanga, namuika m'nyumba yandende chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake Filipo.


Koma pakufika tsiku la kubadwa kwake kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiasi anavina pakati pao, namkondweretsa Herode.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa