Marko 6:18 - Buku Lopatulika18 Pakuti Yohane adanena kwa Herode, Si kuloledwa kwa inu kukhala naye mkazi wa mbale wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pakuti Yohane adanena kwa Herode, Si kuloledwa kwa inu kukhala naye mkazi wa mbale wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndipo Yohane adaamuuza kuti, “Nkulakwira Malamulo kulanda mkazi wa mbale wanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pakuti Yohane ankanena kwa Herode kuti, “Sikololedwa kwa inu kuti mukwatire mkazi wa mʼbale wanu.” Onani mutuwo |