Marko 5:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo pomwepo kasupe wa nthenda yake adaphwa; ndipo anazindikira m'thupi kuti anachiritsidwa chivutiko chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo pomwepo kasupe wa nthenda yake adaphwa; ndipo anazindikira m'thupi kuti anachiritsidwa chivutiko chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Ndipodi nthaŵi yomweyo matenda a msambowo adaleka, mwiniwakeyo nkumva m'thupi mwake kuti matenda ake aja atha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Nthawi yomweyo magazi ake analeka kutuluka ndipo anamva mʼthupi mwake kuti wamasulidwa ku vuto lake. Onani mutuwo |