Marko 5:28 - Buku Lopatulika28 Pakuti ananena iye, Ngati ndikakhudza ngakhale zovala zake ndidzapulumutsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Pakuti ananena iye, Ngati ndikakhudza ngakhale zovala zake ndidzapulumutsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Mumtima mwake ankaganiza kuti, “Ndikangokhudza ngakhale zovala zake zokhazo, ndichira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 chifukwa anaganiza kuti, “Ngati nditangokhudza mkanjo wake, ndidzachiritsidwa.” Onani mutuwo |