Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 3:28 - Buku Lopatulika

28 Indetu, ndinena ndi inu, Adzakhululukidwa machimo onse a ana a anthu, ndi zamwano zilizonse adzachita mwano nazo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Indetu, ndinena ndi inu, Adzakhululukidwa machimo onse a ana a anthu, ndi zamwano zilizonse adzachita mwano nazo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 “Ndithu ndikunenetsa kuti anthu angathe kukhululukidwa machimo onse, ngakhalenso zonena zao zonse zomunyoza Mulunguyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Ndikukuwuzani zoona kuti machimo onse ndi zamwano zonse za anthu zidzakhululukidwa,

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:28
8 Mawu Ofanana  

Ndi iye wakuchitira mwano dzina la Yehova, amuphe ndithu; khamu lonse limponye miyala ndithu; mlendo ndi wobadwa m'dziko yemwe akachitira dzina la Yehova mwano, awaphe.


Ndipo onani, ena a alembi ananena mumtima mwao, Uyu achitira Mulungu mwano.


Ndipo aliyense amene adzanenera Mwana wa Munthu zoipa adzakhululukidwa; koma amene anenera Mzimu Woyera zamwano sadzakhululukidwa.


Wina akaona mbale wake alikuchimwa tchimo losati la kuimfa, apemphere Mulungu, ndipo Iye adzampatsira moyo wa iwo akuchita machimo osati a kuimfa. Pali tchimo la kuimfa: za ililo sindinena kuti mupemphere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa