Marko 15:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo atafika tsono madzulo, popeza mpa tsiku lokonzekera, ndilo la pambuyo pa Sabata, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo atafika tsono madzulo, popeza mpa tsiku lokonzekera, ndilo la pambuyo pa Sabata, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Tsopano chisisira chinali chitagwa. Ndiye popeza kuti linali Lachisanu, tsiku lokonzekera Sabata, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Linali Tsiku Lokonzekera (kunena kuti, tsiku lomwe limatsatizana ndi Sabata). Choncho madzulo atayandikira, Onani mutuwo |