Marko 15:41 - Buku Lopatulika41 amene anamtsata Iye, pamene anali mu Galileya, namtumikira; ndi akazi ena ambiri, amene anakwera kudza ndi Iye ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 amene anamtsata Iye, pamene anali m'Galileya, namtumikira; ndi akazi ena ambiri, amene anakwera kudza ndi Iye ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Azimaiŵa ankatsata Yesu pamene Iye anali ku Galileya, ndi kumamtumikira. Padaalinso azimai ena ambiri omwe adaabwera naye ku Yerusalemuko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Amayi awa ankamutsatira Iye mu Galileya ndi kumutumikira Iye pa zosowa zake. Amayi enanso ambiri amene anabwera naye ku Yerusalemu analinso pomwepo. Onani mutuwo |