Marko 15:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo analinso kumeneko akazi akuyang'anira kutali; mwa iwo anali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo wamng'ono ndi wa Yosefe, ndi Salome; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo analinso kumeneko akazi akuyang'anira kutali; mwa iwo anali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo wamng'ono ndi wa Yosefe, ndi Salome; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Patali poteropo padaali azimai, akungoyang'anitsitsa. Ena mwa iwo anali Maria wa ku Magadala, ndi Maria, mai wa Yakobe wamng'ono uja ndi wa Yosefe, ndiponso Salome. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Amayi ena anali patali kuonerera. Pakati pawo panali Mariya Magadalena, Mariya amayi a Yakobo wamngʼono ndi Yose ndi Salome. Onani mutuwo |