Marko 15:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo iwo akupitirirapo anamchitira mwano, napukusa mitu yao, nanena, Ha! Iwe wakupasula Kachisi, ndi kummanga masiku atatu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo iwo akupitirirapo anamchitira mwano, napukusa mitu yao, nanena, Ha! Iwe wakupasula Kachisi, ndi kummanga masiku atatu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Anthu amene ankadutsa pamenepo ankamunyodola. Ankapukusa mitu nkumanena kuti, “Ha, suja iwe unkati, ‘Ndidzapasula Nyumba ya Mulungu nkuimanganso pa masiku atatu?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Amene amadutsa pafupi anamunenera mawu amwano, akupukusa mitu yawo ndi kuti, “Haa! Iwe amene udzawononga Nyumba ya Mulungu ndi kuyimanganso masiku atatu, Onani mutuwo |