Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 15:27 - Buku Lopatulika

27 Ndipo anapachika pamodzi ndi Iye achifwamba awiri; mmodzi kudzanja lake lamanja ndi wina kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndipo anapachika pamodzi ndi Iye achifwamba awiri; mmodzi kudzanja lake lamanja ndi wina kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Pamodzi ndi Yesu adaapachikanso pa mitanda zigaŵenga ziŵiri, china ku dzanja lamanja, china ku dzanja lamanzere. [

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Achifwamba awiri anapachikidwanso pamodzi ndi Iye, wina kumanja kwake ndi wina kumanzere kwake.

Onani mutuwo Koperani




Marko 15:27
6 Mawu Ofanana  

Pamenepo anapachika pamodzi ndi Iye achifwamba awiri, mmodzi kudzanja lamanja, ndi wina kulamanzere.


Ndipo lembo la mlandu wake linalembedwa pamwamba, MFUMU YA AYUDA.


Atsike tsopano pamtanda, Khristu mfumu ya Israele, kuti tione, ndi kukhulupirira. Ndipo iwo akupachikidwa naye anamlalatira.


kumene anampachika Iye; ndipo pamodzi ndi Iye awiri ena, chakuno ndi chauko, koma Yesu pakati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa