Marko 15:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo panali ora lachitatu, ndipo anampachika Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo panali ora lachitatu, ndipo anampachika Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamene adampachika pa mtanda, nkuti nthaŵi ili 9 koloko m'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Linali ora lachitatu mmawa pamene anamupachika Yesu. Onani mutuwo |