Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 15:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo anampatsa vinyo wosakaniza ndi mure; koma Iye sanamlandire.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo anampatsa vinyo wosanganiza ndi mure; koma Iye sanamlandire.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Adaafuna kumpatsa vinyo wosanganiza ndi mure kuti amwe, koma Iye adakana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Kenaka anamupatsa Iye vinyo wosakaniza ndi mure, koma Iye sanamwe.

Onani mutuwo Koperani




Marko 15:23
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anandipatsa ndulu ikhale chakudya changa; nandimwetsa vinyo wosasa pomva ludzu ine.


Ndipo ophunzira anachita monga Yesu anawauza, nakonza Paska.


anamwetsa Iye vinyo wosakaniza ndi ndulu; ndipo Iye, m'mene analawa, sanafune kumwa.


Ndithu ndinena nanu, Sindidzamwanso chipatso cha mpesa, kufikira tsiku lijalo, limene ndidzamwa icho chatsopano mu Ufumu wa Mulungu.


pakuti ndinena kwa inu, kuyambira tsopano Ine sindidzamwako chipatso cha mpesa, kufikira Ufumu wa Mulungu udzafika.


Ndipo asilikalinso anamnyoza, nadza kwa Iye, nampatsa vinyo wosasa,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa