Marko 15:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anamtenga kunka naye kumalo Gologota, ndiwo, osandulika, Malo a Bade. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anamtenga kunka naye kumalo Gologota, ndiwo, osandulika, Malo a Bade. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Iwowo adapita naye Yesuyo ku malo otchedwa Gologota, (ndiye kuti “Malo a Chibade cha Mutu.”) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anafika naye Yesu pa malo otchedwa Gologota (kutanthauza kuti, malo a bade) Onani mutuwo |