Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 15:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo atatha kumnyoza anamvula chibakuwacho namveka Iye zovala zake. Ndipo anatuluka naye kuti akampachike Iye pamtanda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo atatha kumnyoza anamvula chibakuwacho namveka Iye zovala zake. Ndipo anatuluka naye kuti akampachike Iye pamtanda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Ataseŵera naye mwachipongwe choncho, adamuvula chovala chija, namuvekanso zovala zake. Kenaka adamtenga, nkupita naye kuti akampachike pa mtanda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Ndipo anamuchita chipongwe, anamuvula mwinjiro wofiira uja ndi kumuveka zovala zake. Kenaka anamutenga kuti akamupachike.

Onani mutuwo Koperani




Marko 15:20
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene anatha kumchitira Iye chipongwe, anavula malaya aja, namveka Iye malaya ake, natsogoza Iye kukampachika pamtanda.


Ndipo anampanda Iye pamutu pake ndi bango, namthira malovu, nampindira maondo, namlambira.


Ndipo anakakamiza wina wopitirirapo, Simoni wa ku Kirene, alikuchokera kuminda, atate wao wa Aleksandro ndi Rufu, kuti anyamule mtanda wake.


Ndipo pamenepo anampereka Iye kwa iwo kuti ampachike. Pamenepo anatenga Yesu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa