Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 15:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo anamveka Iye chibakuwa, naluka korona waminga, namveka pa Iye;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo anamveka Iye chibakuwa, naluka korona waminga, namveka pa Iye;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Adamuveka chovala chofiirira, naluka nsangamutu yaminga nkuiika pamutu pake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Anamuveka Iye mwinjiro wofiira, kenaka analuka chipewa cha minga ndi kuyika pa mutu pake.

Onani mutuwo Koperani




Marko 15:17
5 Mawu Ofanana  

Ndipo asilikali anachoka naye nalowa m'bwalo, ndilo Pretorio; nasonkhanitsa gulu lao lonse.


Ndipo anayamba kumlankhula Iye, kuti, Tikuoneni, mfumu ya Ayuda!


Ndipo Herode ndi asilikali ake anampeputsa Iye, namnyoza, namveka Iye chofunda chonyezimira, nambwezera kwa Pilato.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa