Marko 15:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Pilato anawayankhanso, nati kwa iwo, Pamenepo ndidzachita chiyani ndi Iye amene mumtchula mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Pilato anawayankhanso, nati kwa iwo, Pamenepo ndidzachita chiyani ndi Iye amene mumtchula mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono Pilato adaŵafunsanso kuti, “Nanga tsono mukuti ndichite naye chiyani uyu amene mukuti ndi Mfumu ya Ayudayu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pilato anawafunsa kuti, “Kodi nanga ndichite chiyani ndi uyu amene mukumutcha mfumu ya Ayuda?” Onani mutuwo |