Marko 14:71 - Buku Lopatulika71 Koma iye anayamba kutemberera, ndi kulumbira, Sindimdziwa munthuyu mulikunena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201471 Koma iye anayamba kutemberera, ndi kulumbira, Sindimdziwa munthuyu mulikunena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa71 Koma Petro adayamba kudzitemberera nkumalumbira kuti, “Mtheradi, munthu amene mukunenayu ine sindimdziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero71 Iye anayamba kudzitemberera, nalumbira kuti, “Sindimudziwa munthu ameneyu.” Onani mutuwo |