Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 14:52 - Buku Lopatulika

52 koma iye anasiya nsaluyo, nathawa wamaliseche.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 koma iye anasiya bafutayo, nathawa wamaliseche.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 koma iye adaikolopola nsalu ija, nkuthaŵa ali maliseche.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 anathawa wamaliseche kusiya nsalu yake mʼmbuyo.

Onani mutuwo Koperani




Marko 14:52
5 Mawu Ofanana  

Ndipo mkazi anagwira iye chofunda chake, nati, Gona ndi ine; ndipo anasiya chofunda chake m'dzanja lake nathawa, natulukira kubwalo.


Nayankha Satana, nati kwa Yehova, Khungu kulipa khungu, inde munthu adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wake.


Ndipo mnyamata wina anamtsata Iye, atafundira pathupi nsalu yabafuta yokha; ndipo anamgwira;


Ndipo ananka naye Yesu kwa mkulu wa ansembe; ndipo anasonkhana kwa iye ansembe aakulu onse ndi akulu a anthu, ndi alembi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa