Marko 14:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo mnyamata wina anamtsata Iye, atafundira pathupi nsalu yabafuta yokha; ndipo anamgwira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo mnyamata wina anamtsata Iye, atafundira pathupi bafuta yekha; ndipo anamgwira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Mnyamata wina ankatsatira Yesu, atangofundira nsalu yokha, opanda chovala china. Anthu aja adaati amgwire, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Mnyamata wamngʼono amene anangofundira nsalu yokha, wopanda chovala ankamutsatira Yesu. Atamugwira, Onani mutuwo |