Marko 14:47 - Buku Lopatulika47 Koma mmodzi wina wa iwo akuimirirapo, anasolola lupanga lake, nakantha kapolo wake wa mkulu wa ansembe, namdula khutu lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Koma mmodzi wina wa iwo akuimirirapo, anasolola lupanga lake, nakantha kapolo wake wa mkulu wa ansembe, namdula khutu lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Koma wina mwa ophunzira amene anali naye pamenepo, adasolola lupanga lake, natema wantchito wa mkulu wa ansembe onse, mpaka kumusenga khutu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Kenaka mmodzi wa iwo amene anayima pafupipo anatulutsa lupanga lake nakhapa wantchito wa wamkulu wa ansembe, nʼkudula khutu lake. Onani mutuwo |