Marko 14:42 - Buku Lopatulika42 Ukani, tizimuka; onani wakundiperekayo ali pafupi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ukani, tizimuka; onani wakundiperekayo ali pafupi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Dzukani, tiyeni tizipita. Suuyu wodzandipereka uja, wafika.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Nyamukani! Tiyeni tizipita! Uyu wondipereka Ine wafika!” Onani mutuwo |