Marko 14:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anadzanso nawapeza ali m'tulo, pakuti maso ao analemeradi; ndipo sanadziwe chomyankha Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anadzanso nawapeza ali m'tulo, pakuti maso ao analemeradi; ndipo sanadziwe chomyankha Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Pamene adabwerakonso, adaŵapeza ali m'tulo, chifukwa zikope zao zinkalemera ndi tulo. Choncho iwowo adasoŵa choyankha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Iye atabwerera, anawapezanso akugona, chifukwa mʼmaso mwawo munadzaza tulo. Iwo sanadziwe choti anene kwa Iye. Onani mutuwo |