Marko 14:4 - Buku Lopatulika4 Koma anakhalako ena anavutika mtima mwa iwo okha, ndi kuti, Mafutawo atayidwa chifukwa ninji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma anakhalako ena anavutika mtima mwa iwo okha, ndi kuti, Mafutawo atayidwa chifukwa ninji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Anthu ena pamenepo adaipidwa nazo nanena kuti, “Chifukwa chiyani kuŵasakaza chotere mafuta onunkhiraŵa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ena mwa iwo amene analipo, anakwiya nati kwa wina ndi mnzake, “Chifukwa chiyani akuwononga mafuta onunkhirawa? Onani mutuwo |