Marko 14:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo iwo anadza kumalo dzina lake Getsemani; ndipo ananena kwa ophunzira ake, Bakhalani pano, kufikira ndikapemphera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo iwo anadza kumalo dzina lake Getsemani; ndipo ananena kwa ophunzira ake, Bakhalani pano, kufikira ndikapemphera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Yesu adapita ndi ophunzira ake aja ku malo ena, otchedwa Getsemani. Tsono adauza ophunzirawo kuti, “Inu bakhalani pano, Ine ndikukapemphera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Ndipo anapita ku malo otchedwa Getsemani, ndipo Yesu anati kwa ophunzira ake, “Khalani pano pamene Ine ndi kupemphera.” Onani mutuwo |