Marko 14:19 - Buku Lopatulika19 Anayamba iwo kukhala ndi chisoni, ndi kunena naye mmodzimmodzi, kuti, Ndine kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Anayamba iwo kukhala ndi chisoni, ndi kunena naye mmodzimmodzi, kuti, Ndine kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ophunzirawo adamva chisoni, nayamba mmodzimmodzi kumufunsa kuti, “Monga nkukhala ine?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Iwo anamva chisoni, ndipo mmodzi ndi mmodzi anati kwa Iye, “Kodi ndine?” Onani mutuwo |