Marko 13:37 - Buku Lopatulika37 Ndipo chimene ndinena ndi inu ndinena kwa onse, Dikirani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndipo chimene ndinena ndi inu ndinena kwa onse, Dikirani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Zimene ndikunenazi, sindikuuza inu nokha ai, koma ndikuuza anthu onse kuti, ‘Khalani maso.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Zimene ndikunena kwa inu, ndikunena kwa aliyense: ‘Khalani tcheru!’ ” Onani mutuwo |