Marko 13:32 - Buku Lopatulika32 Koma za tsiku ilo, kapena nthawi yake sadziwa munthu, angakhale angelo mu Mwamba, angakhale Mwana, koma Atate ndiye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Koma za tsiku ilo, kapena nthawi yake sadziwa munthu, angakhale angelo m'Mwamba, angakhale Mwana, koma Atate ndiye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 “Koma za tsiku lake kapena nthaŵi yake, palibe amene amadziŵa. Angelo omwe akumwamba sadziŵa. Ngakhale Ineyo Mwanane sindidziŵa, amadziŵa ndi Atate okha basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 “Palibe amene akudziwa za tsikulo kapena nthawi, ngakhale angelo akumwamba, kapena Mwana, koma Atate wokha. Onani mutuwo |