Marko 13:30 - Buku Lopatulika30 Indetu ndinena ndi inu, Mbadwo uno sudzapita kufikira zinthu izi zonse zitachitika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Indetu ndinena ndi inu, Mbadwo uno sudzapita kufikira zinthu izi zonse zitachitika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndithu ndikunenetsa kuti zonsezi zidzaoneka anthu a mbadwo unoŵa asanamwalire onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti mʼbado uno sudzatha mpaka zinthu zonsezi zitachitika. Onani mutuwo |