Marko 13:29 - Buku Lopatulika29 chomwecho inunso, pamene muona zinthu izi zilikuchitika, zindikirani kuti ali pafupi pakhomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 chomwecho inunso, pamene muona zinthu izi zilikuchitika, zindikirani kuti ali pafupi pakhomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Momwemonso mukadzaona zija ndanenazi zikuchitika, mudzadziŵe kuti Mwana wa Munthu ali pafupi, ali pakhomo penipeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Momwenso pamene muona zinthu izi zikuchitika, dziwani kuti wayandikira, ali pa khomo. Onani mutuwo |