Marko 13:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo phunzirani ndi mkuyu fanizo lake; pamene pafika kuti nthambi yake ikhala yanthete, ndipo anaphuka masamba ake, muzindikira kuti layandikira dzinja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo phunzirani ndi mkuyu fanizo lake; pamene pafika kuti nthambi yake ikhala yanthete, ndipo anaphuka masamba ake, muzindikira kuti layandikira dzinja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 “Phunziriraniko kwa mkuyu. Mukamaona kuti nthambi zake zayamba kukhala zanthete ndipo masamba akuphuka, mumadziŵa kuti chilimwe chayandikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 “Tsopano phunzirani phunziro ili kuchokera ku mtengo wamkuyu. Pamene msonga za nthambi zake zikhala za nthete ndipo masamba ake ayamba kuphukira, mumadziwa kuti dzinja layandikira. Onani mutuwo |