Marko 12:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo anadza mkazi wamasiye waumphawi, ndipo iye anaponyamo tindalama tiwiri tating'ono tokwanira kakobiri kamodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo anadza mkazi wamasiye waumphawi, ndipo iye anaponyamo tindalama tiwiri tating'ono tokwanira kakobiri kamodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Koma padafika mai wina wamasiye, wosauka. Iyeyu adangoponyamo tindalama tiŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Koma mkazi wamasiye, wosauka anabwera ndi kuyikamo tindalama tiwiri ta kopala, tongokwanira theka la ndalama. Onani mutuwo |