Marko 12:39 - Buku Lopatulika39 ndi kukhala nayo mipando yaulemu m'sunagoge, ndi malo aulemu pamaphwando: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 ndi kukhala nayo mipando yaulemu m'sunagoge, ndi malo aulemu pamaphwando: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Amakonda mipando yaulemu kwambiri m'nyumba zamapemphero, ndiponso malo olemekezeka pa maphwando. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ndipo amakhala pa mipando yofunika kwambiri mʼmasunagoge ndi malo aulemu pa maphwando. Onani mutuwo |