Marko 12:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo pakuona kuti anayankha ndi nzeru, Yesu anati kwa iye, Suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu. Ndipo palibe munthu analimbanso mtima kumfunsa Iye kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo pakuona kuti anayankha ndi nzeru, Yesu anati kwa iye, Suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu. Ndipo palibe munthu analimbanso mtima kumfunsa Iye kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yesu adaona kuti munthuyo wayankha mwanzeru. Tsono adamuuza kuti, “Iwe suli kutali ndi Ufumu wa Mulungu.” Ndipo kuyambira apo panalibenso wina woti ayesere kumfunsa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu ataona kuti wayankha mwanzeru, anati kwa iye, “Iwe suli kutali ndi ufumu wa Mulungu.” Ndipo kuyambira pamenepo panalibe ndi mmodzi yemwe anayesa kumufunsanso. Onani mutuwo |