Marko 12:23 - Buku Lopatulika23 Pakuuka adzakhala mkazi wa yani wa iwowa? Pakuti asanu ndi awiriwo adamuyesa mkazi wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Pakuuka adzakhala mkazi wa yani wa iwowa? Pakuti asanu ndi awiriwo adamuyesa mkazi wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Nanga tsono pa tsiku lodzauka akufa, mwini mkaziyo adzakhala utiwuti, popeza kuti abale asanu ndi aŵiri onse aja adaamkwatirapo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pa kuuka kwa akufa, adzakhala mkazi wa yani pakuti anakwatiwa ndi onse asanu ndi awiri?” Onani mutuwo |