Marko 12:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, nanena, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, nanena, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambuyo pake Asaduki ena adadza kwa Yesu. Iwo amati akufa sadzauka. Adamufunsa kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka Asaduki, amene amati kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa Iye ndi funso. Onani mutuwo |