Marko 12:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anatuma kwa Iye ena a Afarisi ndi a Aherode, kuti akamkole Iye m'kulankhula kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anatuma kwa Iye ena a Afarisi ndi a Aherode, kuti akamkole Iye m'kulankhula kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Anthu ena a m'gulu la Afarisi, ndi enanso a m'chipani cha Herode, adaatumidwa kuti akatape Yesu m'kamwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pambuyo pake anatuma ena a Afarisi ndi Aherode kwa Yesu kuti adzamukole mawu ake. Onani mutuwo |