Marko 11:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo anatsutsana mwa iwo okha, nanena, Tikati, Kumwamba; adzanena Iye, Ndipo simunakhulupirire iye bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo anatsutsana mwa iwo okha, nanena, Tikati, Kumwamba; adzanena Iye, Ndipo simunakhulupirira iye bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Iwo aja adayamba kukambirana nkumati, “Tikati adaazitenga kwa Mulungu, Iyeyu anena kuti, ‘Nanga bwanji tsono simudamkhulupirire?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Iwo anakambirana pakati pawo ndipo anati, “Tikati, ‘Wochokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga nʼchifukwa chiyani simunamukhulupirire?’ Onani mutuwo |