Marko 11:30 - Buku Lopatulika30 Ubatizo wa Yohane uchokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Mundiyankhe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ubatizo wa Yohane uchokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Mundiyankhe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Kodi Yohane kuti azibatiza, mphamvu zake adaazitenga kwa yani, kwa Mulungu kapena kwa anthu? Tandiyankhani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ubatizo wa Yohane, unali wochokera kumwamba, kapena kwa anthu? Ndiwuzeni.” Onani mutuwo |