Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 11:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ndikufunsani mau amodzi, mundiyankhe Ine, ndipo ndidzakuuzani ulamuliro umene ndichita nao zinthu zimenezi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ndikufunsani mau amodzi, mundiyankhe Ine, ndipo ndidzakuuzani ulamuliro umene ndichita nao zinthu zimenezi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Yesu adati, “Nanenso ntakufunsani funso limodzi. Mukandiyankha, ndiye ndikuuzeni kumene ndidatenga mphamvu zoti ndizichita zimenezi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Yesu anayankha kuti, “Ndikufunsani funso limodzi. Mundiyankhe, ndipo ndikuwuzani ndi ulamuliro wanji umene ndikuchitira izi.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:29
5 Mawu Ofanana  

Taonani, Mtumiki wanga adzachita mwanzeru; adzakwezedwa ndi kutukulidwa pamwamba, nadzakhala pamwambamwamba.


Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Inenso ndikufunsani mau amodzi, amene ngati mundiuza, Inenso ndikuuzani ndi ulamuliro wotani ndizichita izi:


nanena naye, Izi muzichita ndi ulamuliro wotani? Kapena anakupatsani ndani ulamuliro uwu wakuchita izi?


Ubatizo wa Yohane uchokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu? Mundiyankhe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa