Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 11:28 - Buku Lopatulika

28 nanena naye, Izi muzichita ndi ulamuliro wotani? Kapena anakupatsani ndani ulamuliro uwu wakuchita izi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 nanena naye, Izi muzichita ndi ulamuliro wotani? Kapena anakupatsani ndani ulamuliro uwu wakuchita izi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 “Kodi mphamvu zoti muzichita zimenezi mudazitenga kuti? Ndani adakupatsani mphamvu zimenezi?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Iwo anafunsa kuti, “Mukuchita izi ndi ulamuliro wanji? Ndipo anakupatsani ulamuliro umenewu ndi ndani?”

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:28
8 Mawu Ofanana  

Koma anati, Wakuika iwe ndani ukhale mkulu ndi woweruza wathu? Kuteroku ukuti undiphe, monga unamupha Mwejipito? Ndipo Mose anachita mantha, nanena, Ndithu chinthuchi chadziwika.


kodi ndi chinthu chaching'ono kuti watikweza kutichotsa m'dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi, kutipha m'chipululu; koma udziyesanso ndithu kalonga wa ife?


Ndipo anasonkhana motsutsana pa Mose ndi Aroni, nanena nao, Mukula mphamvu inu, pakuti khamu lonse nlopatulika, onsewa, ndipo Yehova ali pakati pao; mudzikuza bwanji pa msonkhano wa Yehova?


Ndipo iwo anadzanso ku Yerusalemu; ndipo m'mene Iye anali kuyenda mu Kachisi, anafika kwa Iye ansembe aakulu, ndi alembi ndi akulu;


Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ndikufunsani mau amodzi, mundiyankhe Ine, ndipo ndidzakuuzani ulamuliro umene ndichita nao zinthu zimenezi.


Ouma khosi ndi osadulidwa mtima ndi makutu inu, mukaniza Mzimu Woyera nthawi zonse; monga anachita makolo anu, momwemo inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa