Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 11:27 - Buku Lopatulika

27 Ndipo iwo anadzanso ku Yerusalemu; ndipo m'mene Iye anali kuyenda mu Kachisi, anafika kwa Iye ansembe aakulu, ndi alembi ndi akulu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndipo iwo anadzanso ku Yerusalemu; ndipo m'mene Iye anali kuyenda m'Kachisi, anafika kwa Iye ansembe aakulu, ndi alembi ndi akulu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Yesu adafikanso ku Yerusalemu. Tsono pamene Iye ankangodziyendera m'Nyumba ya Mulungu, akulu a ansembe ndi aphunzitsi a Malamulo pamodzi ndi akulu a Ayuda adadzamufunsa kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Iwo anafikanso ku Yerusalemu, ndipo pamene Yesu amayenda mʼmabwalo a Nyumba ya Mulungu, akulu a ansembe, aphunzitsi amalamulo ndi akuluakulu anabwera kwa Iye.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:27
10 Mawu Ofanana  

Taonani, ndituma mthenga wanga, kuti akonzeretu njira pamaso panga; ndipo Ambuye amene mumfuna adzadza ku Kachisi wake modzidzimutsa; ndiye mthenga wa chipangano amene mukondwera naye; taonani akudza, ati Yehova wa makamu.


nanena naye, Izi muzichita ndi ulamuliro wotani? Kapena anakupatsani ndani ulamuliro uwu wakuchita izi?


Ndipo popita masiku awiri kuli phwando la Paska ndi Mkate wopanda chotupitsa; ndipo ansembe aakulu ndi alembi anafunafuna momchitira chiwembu, ndi kumupha:


Ndipo Yesu analikuyendayenda mu Kachisi m'khonde la Solomoni.


Yesu anayankha iye, Ine ndalankhula zomveka kwa dziko lapansi; ndinaphunzitsa Ine nthawi zonse m'sunagoge ndi mu Kachisi, kumene amasonkhana Ayuda onse; ndipo mobisika sindinalankhule kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa