Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 11:16 - Buku Lopatulika

16 ndipo sanalole munthu aliyense kunyamula chotengera kupyola pakati pa Kachisi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 ndipo sanalole munthu aliyense kunyamula chotengera kupyola pakati pa Kachisi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Sadalolenso kuti wina aliyense azidutsa m'mabwalo a Nyumbayo atasenza chinthu ai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 ndipo Iye sanalole aliyense kugulitsa malonda mʼmabwalo a Nyumba ya Mulungu.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:16
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anafika iwo ku Yerusalemu; ndipo Iye analowa mu Kachisi, nayamba kutulutsa akugulitsa ndi akugula malonda mu Kachisimo, nagubuduza magome a osinthana ndalama, ndi mipando ya ogulitsa nkhunda;


Ndipo anaphunzitsa, nanena nao, Sichilembedwa kodi, Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yakupempheramo anthu a mitundu yonse? Koma inu mwaiyesa phanga la achifwamba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa