Marko 10:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo Yesu anaima, nati, Mwitaneni. Ndipo anaitana wakhunguyo, nanena naye, Limba mtima; nyamuka, akuitana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo Yesu anaima, nati, Mwitaneni. Ndipo anaitana wakhunguyo, nanena naye, Limba mtima; nyamuka, akuitana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Yesu adaima, nauza anthu kuti, “Tamuitanani.” Anthu aja adamuitana wakhunguyo namuuza kuti, “Limba mtima, nyamuka, akukuitana.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Yesu anayima nati, “Muyitaneni.” Ndipo anamuyitana kuti, “Kondwera! Imirira! Akukuyitana.” Onani mutuwo |