Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 10:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo Iye anati kwa iwo, Mufuna kuti ndidzakuchitireni inu chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo Iye anati kwa iwo, Mufuna kuti ndidzakuchitireni inu chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Yesu adaŵafunsa kuti, “Inuyo mukufuna kuti ndikuchitireni chiyani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Iye anafunsa kuti, “Kodi mukufuna ndikuchitireni chiyani?”

Onani mutuwo Koperani




Marko 10:36
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anadza kwa Iye Yakobo ndi Yohane, ana a Zebedeo, nanena naye, Mphunzitsi, tifuna kuti mudzatichitire chimene chilichonse tidzapempha kwa Inu.


Ndipo iwo anati kwa Iye, Mutipatse ife kuti tikhale mmodzi kudzanja lanu lamanja, ndi wina kulamanzere, mu ulemerero wanu.


Ndipo Yesu anamyankha, nati, Ufuna kuti ndikuchitire chiyani? Ndipo wakhunguyo anati kwa Iye, Raboni, ndilandire kuona kwanga.


Ngati mukhala mwa Ine, ndi mau anga akhala mwa inu, pemphani chilichonse chimene muchifuna ndipo chidzachitika kwa inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa