Marko 10:31 - Buku Lopatulika31 Koma ambiri akuyamba adzakhala akuthungo, ndi akuthungo adzakhala oyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma ambiri akuyamba adzakhala akuthungo, ndi akuthungo adzakhala oyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Komatu ambiri amene ali oyambirira adzakhala otsirizira, ndipo amene ali otsirizira adzakhala oyambirira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Koma ambiri amene ndi woyambirira adzakhala omalizira, ndipo omalizira adzakhala oyambirira.” Onani mutuwo |