Marko 10:28 - Buku Lopatulika28 Petro anayamba kunena naye, Onani, ife tinasiya zonse, ndipo tinakutsatani Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Petro anayamba kunena naye, Onani, ife tinasiya zonse, ndipo tinakutsatani Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Pamenepo Petro adayamba kulankhula naye, adati, “Ifetu paja tidasiya zonse kuti tizikutsatani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Petro anati kwa Iye, “Ife tasiya zonse ndi kukutsatani!” Onani mutuwo |