Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 5:9 - Buku Lopatulika

9 Timalowa m'zoopsa potenga zakudya zathu, chifukwa cha lupanga la m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Timalowa m'zoopsa potenga zakudya zathu, chifukwa cha lupanga la m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pofunafuna chakudya, timagwa m'zoopsa chifukwa cha anthu opha anzao ku chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Timapeza chakudya chathu poyika miyoyo yathu pa chiswe chifukwa cha lupanga mʼchipululu.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 5:9
9 Mawu Ofanana  

Nati, Ndisachite ichi ndi pang'ono ponse, Yehova; ndimwe kodi mwazi wa anthu awa anapitawa ndi kutaya moyo wao? Chifukwa chake iye anakana kumwa. Izi anazichita ngwazi zitatuzi.


chifukwa cha Ababiloni; pakuti anawaopa, chifukwa Ismaele mwana wake wa Netaniya anapha Gedaliya mwana wake wa Ahikamu, amene mfumu ya ku Babiloni anamuika wolamulira m'dzikomo.


ndi kuti, Iai; tidzanka ku Ejipito, kumene sitidzaona nkhondo, sitidzamva kulira kwa lipenga, sitidzamva njala yokhumba mkate; pamenepo tidzakhala;


pamenepo padzakhala, kuti lupanga limene muopa lidzakupezani m'menemo m'dziko la Ejipito, ndi njala, imene muiopa, idzakuumirirani kumeneko ku Ejipito; pamenepo mudzafa.


Pamenepo anadza mthenga wa Yehova, nakhala patsinde pa thundu wokhala mu Ofura, wa Yowasi Mwabiyezere; ndi mwana wake Gideoni analikuomba tirigu m'mopondera mphesa, awabisire Amidiyani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa