Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Maliro 5:11 - Buku Lopatulika

11 Anaipitsa akazi mu Ziyoni, ndi anamwali m'midzi ya Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Anaipitsa akazi m'Ziyoni, ndi anamwali m'midzi ya Yuda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ku Ziyoni akazi akuŵachita zadama mwakhakhamizo. M'mizinda ina ya ku Yuda anamwali akuŵachita chimodzimodzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Amayi agwiriridwa mu Ziyoni, ndi anamwali mʼmizinda ya Yuda.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 5:11
3 Mawu Ofanana  

Makanda ao adzatswanyidwe pamaso pao; m'nyumba mwao mudzafunkhidwa, ndi akazi ao adzakakamizidwa.


Pakuti ndidzasonkhanitsa amitundu onse alimbane ndi Yerusalemu; ndipo mzindawo udzalandidwa, ndi nyumba zidzafunkhidwa, ndi akazi adzakakamizidwa; ndi limodzi la magawo awiri la mzinda lidzatuluka kunka kundende, koma anthu otsala sadzaonongeka m'mzindamo.


Mudzapalana ubwenzi ndi mkazi, koma mwamuna wina adzagona naye; mudzamanga nyumba, osakhala m'mwemo; mudzaoka munda wampesa, osalawa zipatso zake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa